Malawi Music Logo

Malawi-Music.com

Nyimbo Zachimalawi, Mobile Version

Alex Chungah

Bio:
Alex Chungah, from Nkhamenya Kasungu, T/A Kalulua. Nnabadwira ku Queen Elizabeth, third born, ndaimbapo ndi The burning arrows imene imasogozedwa ndi Wisdom Gondwe komanso Heatherwick Msiska, nnayamba kuimba ndili 13/14 yrs, ndatulutsapo Album yotchedwa NDANYAMULA MFUMU imene yagulidwa bwino kwambiri mu dziko la South Africa and pano Ma cd akupezeka ku Lilongwe. Alex amakonda kumvera Ndilande Anglican chifukwa cha Denis Kalimbe, komanso Lloyd Phiri ndi Skeffa Chimoto. Ku SA kuli Lundi Tyamala ndi Dumi.

Added to site: 2017-01-04 13:41:18

Albums by Alex Chungah